21 Cifukwa cace atero Yehova, Taona, ndidzaikira anthuwa zopunthwitsa; ndipo atate ndi ana adzakhumudwa nazo pamodzi; munthu ndi mnzace adzatayika.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 6
Onani Yeremiya 6:21 nkhani