Yeremiya 6:4 BL92

4 Lalikirani nkhondo yakumenyana ndi iye; ukani, tikwere pakati pa usana. Tsoka kwa ife! pakuti dzuwa lapendeka, mithunzi ya madzulo yatambasuka.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 6

Onani Yeremiya 6:4 nkhani