Yeremiya 7:2 BL92

2 Ima m'cipata ca nyumba ya Yehova, lalikira m'menemo mau awa, ndi kuti, Tamvani mau a Yehova, inu nonse a Yuda, amene alowa m'zipata izi kuti mugwadire Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 7

Onani Yeremiya 7:2 nkhani