23 koma cinthu ici ndinawauza, kuti, Mverani mau anga, ndipo ndidzakhala Mulungu wanu, ndipo inu mudzakhala anthu anga; nimuyende m'njira yonse imene ndakuuzani inu, kuti cikukomereni.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 7
Onani Yeremiya 7:23 nkhani