Yeremiya 8:17 BL92

17 Pakuti, taonani, ndidzatumiza pa inu njoka, mphiri, zosalola kuitanidwa; ndipo zidzakulumani inu, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 8

Onani Yeremiya 8:17 nkhani