Yeremiya 8:3 BL92

3 Ndipo otsala onse amene akutsala pa banja loipa ili adzasankha imfa koposa moyo, ndiwo amene atsala m'malo monse m'mene ndinawaingiramo, ati Yehova wa makamu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 8

Onani Yeremiya 8:3 nkhani