4 Mucenjere naye yense mnansi wace, musakhulupirire yense mbale wace; pakuti abale onse amanyenga, ndipo anansi onse adzayenda ndi maugogodi.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 9
Onani Yeremiya 9:4 nkhani