6 Ndipo Yehova anati kwa ine, Lalikira mau onsewa m'midzi ya Yuda, ndi m'miseu ya Yerusalemu, kuti, Tamvani mau a pangano ili, ndi kuwacita.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 11
Onani Yeremiya 11:6 nkhani