27 Ndaona zonyansa zako, ndi zigololo zako, ndi zakumemesa zako, ndi cinyerinyeri ca dama lako, pamapiri ndi m'munda. Tsoka kwa iwe, Yerusalemu! Sudzayeretsedwa; kodi zidzatero mpaka liti?
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 13
Onani Yeremiya 13:27 nkhani