Yeremiya 13:4 BL92

4 Tenga mpango umene unaugula, umene uli m'cuuno mwako, nuuke, nupite ku Firate, nuubise m'menemo m'phanga la m'mwala.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 13

Onani Yeremiya 13:4 nkhani