Yeremiya 15:17 BL92

17 Sindinakhala m'msonkhano wa iwo amene asekera-sekera, ndi kusangalala; ndinakhala pandekha cifukwa ca dzanja lanu; pakuti mwandidzaza ndi mkwiyo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 15

Onani Yeremiya 15:17 nkhani