20 ndipo uziti kwa iwo, Tamvani mau a Yehova, inu mafumu a Yuda, ndi Ayuda onse, ndi onse okhala m'Yerusalemu, amene alowa pa zipatazi;
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17
Onani Yeremiya 17:20 nkhani