5 Atero Yehova: Wotembereredwa munthu amene akhulupirira munthu, natama mkono wanyama, nucoka kwa Yehova mtima wace.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17
Onani Yeremiya 17:5 nkhani