Yeremiya 17:6 BL92

6 Ndipo adzakhala ngati tsanya la m'cipululu, ndipo saona pamene cifika cabwino; koma adzakhala m'malo oumitsa m'cipululu, dziko lacikungu lopanda anthu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17

Onani Yeremiya 17:6 nkhani