Yeremiya 19:14 BL92

14 Pamenepo Yeremiya anadza kucokera ku Tofeti, kumene Yehova anamtuma iye kuti anenere; ndipo anaima m'bwalo la nyumba ya Yehova, nati kwa anthu onse:

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 19

Onani Yeremiya 19:14 nkhani