Yeremiya 19:15 BL92

15 Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli atero, Taonani, ndidzatengera mudzi uwu ndi midzi yace yonse coipa conse cimene ndaunenera; cifukwa anaumitsa khosi lao, kuti asamve mau anga.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 19

Onani Yeremiya 19:15 nkhani