Yeremiya 20:1 BL92

1 Ndipo Pasuri mwana wace wa Imeri wansembe, amene anali kapitao wamkuru m'nyumba ya Yehova, anamva Yeremiya alikunenera zimenezi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 20

Onani Yeremiya 20:1 nkhani