2 Ndipo Pasuri anampanda Yeremiya mneneriyo, namuika matangadza amene anali m'cipata ca kumtunda ca Benjamini, cimene cinali ku nyumba ya Yehova.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 20
Onani Yeremiya 20:2 nkhani