Yeremiya 19:5 BL92

5 namanga misanje ya Baala, kuti apsereze ana ao m'menemo nsembe zopsereza za Baala, cimene sindinawauza, sindinacinena, sicinalowa m'mtima mwanga;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 19

Onani Yeremiya 19:5 nkhani