Yeremiya 19:6 BL92

6 cifukwa cace, taonani, masiku adza, ati Yehova kuti pamalo pano sipadzachedwanso Tofeti, kapena Cigwa ca mwana wace wa Hinomu, koma Cigwa Cophera anthu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 19

Onani Yeremiya 19:6 nkhani