Yeremiya 22:15 BL92

15 Kodi udzakhala mfumu, cifukwa iwe uyesa kuposa ena ndi mikungudza? Kodi atate wako sanadya ndi kumwa, ndi kuweruza molungama? kumeneko kunamkomera.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22

Onani Yeremiya 22:15 nkhani