Yeremiya 22:14 BL92

14 amene ati, Ndidzadzimangira ndekha nyumba yotakata ndi zipinda zapamwamba zazikuru, nadziboolera mazenera; nabvundima chindwi lam'kati ndi mikungudza, naipaka ndi utoto wofiira.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22

Onani Yeremiya 22:14 nkhani