13 Tsoka iye amene amanga nyumba yace ndi cisalungamo, ndi zipinda zapamwamba ndi cosaweruza bwino; amene agwiritsa mnzace nchito osamlipira, osampatsa mphotho yace;
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22
Onani Yeremiya 22:13 nkhani