22 Mphepo idzadyetsa abusa ako onse, ndipo mabwenzi ako adzalowa m'ndende; ntheradi udzakhala ndi manyazi ndi kunyazitsidwa cifukwa ca coipa cako conse.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22
Onani Yeremiya 22:22 nkhani