23 Iwe wokhala m'Lebano, womanga cisa cako m'mikungudza, udzacitidwa cisoni cacikuru nanga pamene mapweteko adzadza kwa iwe, monga mkazi alinkudwala!
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22
Onani Yeremiya 22:23 nkhani