Yeremiya 22:24 BL92

24 Pali ine, ati Yehova, ngakhale Koniya mwana wace wa Yehoyakimu mfumu ya Yuda akadakhala mphete ya pa dzanja langa lamanja, ndikadacotsa iwe kumeneko;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22

Onani Yeremiya 22:24 nkhani