20 Mkwiyo wa Yehova sudzabwerera, mpaka atacita, mpaka atatha maganizo a mtima wace; masiku otsiriza mudzacidziwa bwino.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23
Onani Yeremiya 23:20 nkhani