Yeremiya 23:21 BL92

21 Sindinatuma aneneri awa, koma anathamanga; sindinanena ndi iwo, koma ananenera.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:21 nkhani