Yeremiya 23:3 BL92

3 Ndipo ndidzasonkhanitsa zotsala za zoweta zanga za m'maiko onse m'mene ndinazipitikitsiramo, ndipo ndidzazitengeranso ku makola ao; ndipo zidzabalana ndi kucuruka.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:3 nkhani