Yeremiya 24:7 BL92

7 Ndipo ndidzapatsa iwo mtima wakundidziwa, kuti ndine Yehova; nadzakhala anthu anga, ndipo Ine ndidzakhala Mulungu wao; pakuti adzabwera kwa Ine ndi mtima wao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 24

Onani Yeremiya 24:7 nkhani