15 Pakuti Yehova, Mulungu wa Israyeli, atero kwa ine, Tenga cikho ca vinyo wa ukaliwu pa dzanja langa, ndi kumwetsa mitundu yonse, imene ndikutumizirako.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25
Onani Yeremiya 25:15 nkhani