Yeremiya 25:28 BL92

28 Ndipo padzakhala, ngati akana kutenga cikho pa dzanja lako kuti amwe, uziti kwa iwo, Yehova wa makamu atero: Kumwa muzimwa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25

Onani Yeremiya 25:28 nkhani