5 Ndipo Yeremiya mneneri anati kwa Hananiya mneneri pamaso pa ansembe, ndi pamaso pa anthu onse amene anaima m'nyumba ya Yehova,
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 28
Onani Yeremiya 28:5 nkhani