19 Ndipo padzaturuka pa izo mayamikiro ndi mau a iwo okondwerera; ndipo ndidzacurukitsa iwo, sadzakhala owerengeka; ndidzawacitiranso ulemu, sadzacepa.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 30
Onani Yeremiya 30:19 nkhani