Yeremiya 30:20 BL92

20 Ana aonso adzakhala monga kale, ndipo msonkhano wao udzakhazikika pamaso panga, ndipo ndidzalanga onse amene akupsinja iwo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 30

Onani Yeremiya 30:20 nkhani