Yeremiya 31:22 BL92

22 Udzayenda kwina ndi kwina masiku angati; iwe mwana wamkazi wobwerera m'mbuyo? pakuti Yehova walenga catsopano m'dziko lapansi: mkazi adzasanduka mphongo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:22 nkhani