7 Pakuti Yehova atero, Yimbirirani Yakobo ndi kukondwa, pfuulirani mtundu woposawo; lalikirani, yamikirani, ndi kuti, Yehova, mupulumutse anthu anu, ndi otsala a Israyeli,
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31
Onani Yeremiya 31:7 nkhani