1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova caka cakhumi ca Zedekiya mfumu ya Yuda, cimene cinali caka cakhumi ndi cisanu ndi citatu ca Nebukadirezara.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32
Onani Yeremiya 32:1 nkhani