2 Nthawi yomweyo nkhondo ya mfumu ya Babulo inamangira Yerusalemu misasa; ndipo Yeremiya mneneri anatsekeredwa m'bwalo la kaidi, linali ku nyumba ya mfumu ya Yuda.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32
Onani Yeremiya 32:2 nkhani