30 Pakuti ana a Israyeli ndi ana a Yuda anacita zoipa zokha zokha pamaso panga ciyambire ubwana wao, pakuti ana a Israyeli anandiputa Ine kokha kokha ndi nchito ya manja ao, ati Yehova.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32
Onani Yeremiya 32:30 nkhani