36 Cifukwa cace tsopano atero Yehova, Mulungu wa Israyeli, za mudzi umene, munena inu, waperekedwa m'dzanja la mfumu ya Babulo ndi lupanga, ndi njala, ndi caola:
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32
Onani Yeremiya 32:36 nkhani