20 Ngati mukhoza kuswa pangano langa la usana ndi pangano langa la usiku, kuti usakhalenso usana ndi usiku m'nyengo yao;
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 33
Onani Yeremiya 33:20 nkhani