21 pamenepo pangano langa lidzasweka ndi Davide mtumiki wanga, kuti asakhale ndi mwana wamwamuna wakulamulira pa mpando wa ufumu wace; ndiponso ndi Alevi ansembe, atumiki anga.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 33
Onani Yeremiya 33:21 nkhani