Yeremiya 35:13 BL92

13 Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Pita, nunene kwa anthu a Yuda ndi kwa okhala m'Yerusalemu, Kodi simudzalola kulangizidwa kumvera mau anga ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 35

Onani Yeremiya 35:13 nkhani