Yeremiya 36:28 BL92

28 Tenganso mpukutu wina, nulembe m'menemo mau oyamba aja anali mu mpukutu woyamba uja, umene Yehoyakimu mfumu ya Yuda wautentha.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:28 nkhani