Yeremiya 36:8 BL92

8 Ndipo Baruki mwana wa Neriya anacita monga mwa zonse anamuuza iye Yeremiya mneneri, nawerenga m'buku mau a Yehova m'nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:8 nkhani