7 Kapena pembedzero lao lidzagwa pamaso pa Yehova, ndipo adzabwerera yense kuleka njira yace yoipa; pakuti mkwiyo ndi ukali umene Yehova wanenera anthu awa ndi waukuru.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36
Onani Yeremiya 36:7 nkhani