Yeremiya 38:19 BL92

19 Ndipo mfumu Zedekiya anati kwa Yeremiya, Ine ndiopa Ayuda amene anandipandukira ine kunka kwa Akasidi, angandipereke ine m'manja mwao, angandiseke.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 38

Onani Yeremiya 38:19 nkhani