Yeremiya 38:28 BL92

28 Ndipo Yeremiya anakhala m'bwalo la kaidi mpaka dzuwa lakugwidwa Yerusalemu. Ndipo anali komweko pogwidwa Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 38

Onani Yeremiya 38:28 nkhani