Yeremiya 38:27 BL92

27 Ndipo akuru onse anadza kwa Yeremiya, namfunsa; ndipo iye ananena nao monga mwa mau onsewo anamuuza mfumu. Ndipo analeka kunena naye; pakuti sikunamveka mlandu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 38

Onani Yeremiya 38:27 nkhani